We use cookies to enhance your browsing experience and to improve the performance of our website. By continuing to use our site, you consent to our use of cookies. You can learn more about our cookie policy & privacy-policy.
Mr Mzaliwa - Basi (Prod. Dry B & Me Qelito) - Mr Mzaliwa - Basi (Prod. Dry B & Me Qelito) lyrics
Mr Mzaliwa - Basi (Prod. Dry B & Me Qelito) | Mr Mzaliwa - Basi (Prod. Dry B & Me Qelito) Lyrics
[INTRO] Itâs a king Wa Malawi oohyeah..!! / Mr Ayaya..!!! (Verse 1) Ukamwetulira mtimawu / Dhu-Dhu kugunda / Ukasekelera nthupili / Paliponse kukoma / You look so credible / You the one I love / Para nakusowa vikwenda yayi / Darling ndiwe moyo wa ine / Ukatalikira ndi madwala / Nkhukupenjanga mazuwa yonse / Mawazo ikundivuta / Ndakumisingâa masiku onse / Ndiwe provider / Ndiwe chitetezo cha ine / Undipatse mpata / Ndikukonde mpaka mapeto /
[HOOK] Tenga zanga zonse basi â¦!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi â¦!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo â¦!!! Usamasowe â usamasowe Umandikonderamo â¦!!! Usamasowe â usamasowe
(Verse 2) Ungasowanga yaye / Ishi na mimi / Uwenge nane / Niwewe pekee / Ndimafuna love ya kanthinthi / Yosawona nyengo / Undisambizye mwantinti / Mopanda zilango / [HOOK] Tenga zanga zonse basiâ¦!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basiâ¦!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe (Verse 3) Zomwe ine ndinkakhumba / Ndazipeza zili mwa iwe / Aka ndi kanga kanga / Palibeso oposa iwe / Zafika ndikuthangatire babe / Bwera kuno ndikunyadire / Zikavuta usandilalatire hunie / Mwachikondi undilakhule / Wewe ni mwanga / Katika maisha yangu / Ninakuhitaji kila siku / Wewe ni moyo wangu / Unanipa furaha hata / Ukiwa mbali / Kulikonse tingapite apa / Tili awiri /
[HOOK] Tenga zanga zonse basiâ¦!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basiâ¦!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe
[HOOK] Tenga zanga zonse basiâ¦!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basiâ¦!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe Umandikonderamoâ¦!!! Usamasowe â usamasowe