Cartlage Don - fade-away mp3 download

Artist: Cartlage Don

  • Genre: Afrobeat
  • Duration: 03:04 min
  • Size: 7.12 MB
  • Album: Single
  • Plays: 1098
  • 2023

Cartlage Don - fade-away Song Description

The song is about a boy/girl who has dreams while younger and realized that life is more than dream and that dream die as you grow older..

fade-away Song Lyric

Iye iye iyeee Cartlage don ALL 4 ALL Verse 1 ndimakumbukila naneso ndili mwana Ndinali ndizofuna/

Ndimakumbukila naneso ndili mwana ndinali ndimaloto/

Nane ndimkafuna nditavaya uptown/ Straight from the ghetto ndikakhale ding ding/

Nane ndimkafuna nditakhala ngat simbi Zadzina langa lidzadziwe mkhimbi/

Koma sindimkadziwa mama Dziko ndichan/ Sindimkadziwa mama mawa libalanji/

Hook: Zomwe Ndimafunaaa Sizomwe ndimapeza/ Zomwe ndimalota Sizomwe zimabwela/

Dreams fade away Maloto amafaaaaa/ x2

Verse 2: Naye amkafuna adzamange oyera Save the date a day to remember/ 

Naye amkafuna adzakhale ogera Ali mu gown ndizomwe amkafuna/

Koma kunabwera Ena anampatsa phaaa Pano ndi baby mama/ Kunabwera imfa inadzatenga msanamila School sanapite/ Sizomwe amkafuna kukhala oyenda yenda/

Sizomwe amkafuna kudzakhala chidakwa/ Sizomwe amkafunaaaaaaa Sizomwe amkalotaaaa/

Hook Zomwe Ndimafunaaa Sizomwe ndimapeza/

Zomwe ndimalota Sizomwe zimabwela/ Dreams fade away Maloto amafaaaaa/ x2 Bridge Zomwe amkafuna sizomwe anapeza Ndiye moyo (Ndiye moyo)/

Zomwe amkalota sizomwe zimabwela Ndiye moyo (ndiye moyo)/

Life ah nuh easy Life ah nuh movie Life ah nuh easy... Life ah nuh movie...yeah... Hook Zomwe Ndimafunaaa Sizomwe ndimapeza/

Zomwe ndimalota Sizomwe zimabwela/ Dreams fade away Maloto amafaaaaa/ x2

Comments (0)

What do you think of this song fade-away ?: