We use cookies to enhance your browsing experience and to improve the performance of our website. By continuing to use our site, you consent to our use of cookies. You can learn more about our cookie policy & privacy-policy.
*VERSE 2* Sizikupanga chipongwe anthu panopo si zi kufwamba/ ndatopa kuphula njerwa ndikufuna ndizatole chikwama/ struggle mu ghetto si ti ma kazinga chakudya timawilitsa/ water mu kettle ku yi khwidzinga kenako madzi kuphitsa/ ukwati wa dzulo uja kucha kwa lero akuti watha/ ndalama za chipatala zija akuti aba zatha/ zaka zaka zikupita koma moyo osamasintha/ bolanso weather umadziwa kuti summer kenako winter/ ndatopa nazo