We use cookies to enhance your browsing experience and to improve the performance of our website. By continuing to use our site, you consent to our use of cookies. You can learn more about our cookie policy & privacy-policy.
Tsar Leo - Misonzi ft Teddy (Prod. Ckay & Mwanie) - Tsar Leo - Misonzi ft Teddy (Prod. Ckay & Mwanie) lyrics
Tsar Leo - Misonzi ft Teddy (Prod. Ckay & Mwanie) | Tsar Leo - Misonzi ft Teddy (Prod. Ckay & Mwanie) Lyrics
Verse 1
Baby Mtima wanga unautenga Ndipo mzimu wanga unavomera Ndisaname unkandipatsachimwemwe eh There was only you, ndimapanga za iwe Mami Mami unandiswera Mtima wanga Mami mami utandibera Mtima wanga I was convinced kuti ndapeza Mtima wanga wadekha.
âHook Nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4
âVerse 2 Mesa unkandikonda? Ine ndinkakukonda baby Ife tinkakondana , atleast that's what I thought Oh baby How did we end up here eh? Olo unandisaya bae ,Ndinkakukonda x2 Panopa nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4
âBridge Unandisya Misonzi x 8
âHook Nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4